Was expecting jimmy ndithhhuu to be the doctors boyfriend 🤣🤣🤣🤣
I know kuti azimai ndi atsikana ambiri malangizo adotolo wo sawakonda komabe ndi khaaa!! Khaa!! Khaaaa!!! Kachilungamo basi
Jimmy akupanga zinthu eee😂😂
Kkk kma yah zikubeba guys....more fire ❤
Unfortunately am in love with fiona❤❤my cool actress
The entanglements in this movie 🤣🙌
Azimai bwerani pano adotolo akurankhura kt chashimuna shilishotse ankazi 4 or 8
Komanso this little sister of Richard is something else😂😂😂
😂😂. Dan ndi Richard azapanga za sikusinja ndi gwenembe ndithu 😂😂🔥🔥..next part plz musamachedwe bundle yanthu tumagula fukwa cha inu
Exactly what I was expecting 🤣🤣🤣🤣 kuti handsome man yo ndi Jimmy , doctor's fiance 😂
Mkkķk dan ndiwachibwana bwanji kkkkk mkhani osaona nthawi yobweletsepa
Richard is my best guys😅 eee big up brother❤
Ati ndikasangalala nthawi zina ndimamwako😂 osangoti ndiwe mbiya ng'ambe bwanji
Guys nkhani zokoma ngati izii mmazibisaa kuti,, eeish this is so perfect, but Dan will not kill me oh😂😂😂❤ bravo! Jnr Scot❤
Iyi ndi imene inawula series iyi kwa ine pa fb anaponya wina wake wamdalitso
Honestly these series makes my day always. I watch every day
Aunt awa amamulangiza fiona koma mene akumuyankhulira boyfriend wawowo mmmmmmm🤣🤣🤣🤣🤣
❤inuyo mwabwera kudzakhala please can't wait part episode 13
😂😂😂 Ati zapwanyila pakaz wake yemweyo
@keifa6652